Download sounds clips for free

Weather

Dzuwa - Sun
Mvula - Rain
Mphepo - Wind
Chivomerezi - Earthquake

Relatives/People

Father – Abambo
Mother – Amayi
Brother – Achimwene
Sister – Asisi
Sister in Law – Alamu
Brother in Law – Apongozi
Child/baby – mwana
Girl – mkazi
Boy – mwamuna
Respected person – Achikulire
Elder Person – agogo
Chief – mfumu
People – Anthu

Questions/Gestures

When? – Liti?
What? – Chiyani?
Where? – Kuti?
Why? – Chifukwa chiyani?
How? – Bwanji?
Case/Dispute – mlandu “
Okay – Chabwino
Yes – inde / eya
No – ayi / iyayi
Now – tsopano
Maybe – kapena
Try – Yesa

Home

House – Nyumba
Garden – munda
Door – chitseko
Roof – Denga
Window – Galasi/Window
Open – Tsegula
Close – Tseka
Road – Nsewu
Car – galimoto
English lang – Chingelezi

Areas/Items

Market – msika
Too Expensive – Zachuluka
European* – mzungu
School – sukulu
Teacher – mphunzitsi
Market – msika
Chair – mpando
Luggage – katundu
Money – ndalama
How Much? – Ndalama zingati?
Church – tchalitchi
God – Mulungu
Lord – Ambuye
Stream – mtsinje
Lake – nyanja

Time/Referrals

Today – lero
Tomorrow – mawa
Yesterday – Dzulo
Day before Yesterday – Dzana
Day – tsiku
Yesterday – dzulo
Week – sabata
Month – Mwezi
Monday – Lolemba
Tuesday – Lachiwiri
Wednesday – Lachitatu
Thursday – Lachinayi
Friday – Lachisano
Saturday – Loweruka
Sunday – Lamulungu
Here, on this spot – pano
There, over there – uko
Here, generally – kuno
In there – Umo
That side/There – Uko

Food

Chokudya – Food
Ludzu – Thirsty
Mowa – Alcohol
Fodya – Cigarettes
Mkaka – Milk
Mazira – Eggs
Nyama – Meat
Ufa – Corn Flour
Chimanga – Ufa
Mafuta – Oil
Mandimu – Lemons
Lalanje – Orange
Nthochi – Bananna
Mango – Mango

Animals/Creatures

Fish – Nsomba
Snake – Njoka
Kalulu – Rabbit
Njovu – Elephant
Mkango – Lion
Mbalame – Bird
N’gona – Crocodile
Mvuu – Hippo
Khuku – Chicken
N’gombe – Cow
Mbuzi – Goat
Galu – Dog
Mphaka – Cat
Khoswe – Rat
Udzuzu – Mosquito
Nkhwere – Baboon
Nyani – Monkey

Clothes

Zovala – Clothes
Shati – Shirt
Kabudula – Shorts
Sokosi – Socks
Thaluwuza – Trousers
Dilesi – Dress
Chipewa – Hat

Kitchen Ware

Mpeni – Knife
Foloko – Fork
Sipuni – Spoon
Tambula – Tumbler/Glass
Kuweza – Fishing

Nature/Equipment

Maluwa – Flower
Mtengo – Tree
Thengo – Forest/Bush
Khasu – Hoe

Sickness and Disease

Malaria – malungo
Cough – chifuwa
Flu/Cold – Chimfine
Medicine – mankhwala
Diarrhea – kutsekula mmimba
Tuberculosis – chifuwa chachikulu
Sick – kudwala

Sentences

How are you? – Muli bwanji?
I’m fine. (What about you?) – Ndili bwino. (Kaya inu?)
How are you this morning? – Mwadzuka bwanji?
I’m fine this morning. (What about you?) – Ndadzuka bwino. (Kaya inu?)
Mwaswera bwanji? – How are you this afternoon?
I’m fine this afternoon. (What about you?) – Ndaswera bwino. (Kaya inu?)
Where are you going? – Mukupita kuti?
I’m going to ______. – Ndikupita ku ______.
Ndikuyendayenda. – I’m just walking around.
Where have you come from? – Mwachokera kuti?
I’ve come from ______. – Ndachokera ku ______.
Tionana! – We shall meet! (‘See you later!’)
I’m going! – Ndapita!
Go well! – Muyende bwino! / Yendani bwino!
Stay well! – Mutsale bwino! / Tsalani bwino!
What’s your name? – Dzina lanu ndani?
My name is ______. – Dzina langa ndi ______.
What do you want/need? – Mufuna chiyani?
Who do you want/need? – Mufuna ndani?
I want……………… – Ndimafuna…………
This – Ichi
That – Icho
Where is ______? – ______ ali kuti?
What time is it? – Nthawi ili bwanji?
At what time? – Nthawi yanji?
Thank you (very much).– Zikomo (kwambiri).
Sorry! – Pepani!
I don’t understand. – Sindikumvetsa.
I don’t speak much Chichewa. – Sindimamvetsa kwambiri Chichewa.
It happens! – Zimachitika.
Take my picture! – Mundijambule! / Jambulani!
Give me money. – Mundipatse ndalama.
How much is it? – Ndi Zingati
Give me sweets. – Mundipatse maswiti.
I don’t have ______ – Ndilibe ______.
I would like (This) – Ndikufuna (Ichi)
You (to an elder) – Inu
You (Younger than you) – Iwe
Why? – Chifukwa
I don’t want. – Sindikufuna
I would like. – Ndikufuna
Go (when sending someone) – Ta Pitani
I’ve arrived – Ndafika
Come here. – Ta bwerani
Please – Chonde

Expressions

Aaaaa – Never, no ways, you must be joking…
Eeeee – Wow
Iiiii – Warning or surprise shock
Shapu – How is it?

Vowel Pronunciation

A = Ah
E = A
I = E
O = O
U = Uuu